Salimo 88:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Anzanga mwawathamangitsira kutali ndi ine.+Mwandipangitsa kuti ndikhale chinthu chonyansa kwa iwo. Ndakodwa ndipo sindingathe kuthawa.
8 Anzanga mwawathamangitsira kutali ndi ine.+Mwandipangitsa kuti ndikhale chinthu chonyansa kwa iwo. Ndakodwa ndipo sindingathe kuthawa.