Yobu 17:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Iye wachititsa kuti anthu azindinyoza,+Mwakuti ndakhala munthu amene anthu akumulavulira kumaso.+ Salimo 88:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Anzanga mwawathamangitsira kutali ndi ine.+Mwandipangitsa kuti ndikhale chinthu chonyansa kwa iwo. Ndakodwa ndipo sindingathe kuthawa.
8 Anzanga mwawathamangitsira kutali ndi ine.+Mwandipangitsa kuti ndikhale chinthu chonyansa kwa iwo. Ndakodwa ndipo sindingathe kuthawa.