Yobu 16:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Anthu atsegula kukamwa kwawo kuti andimeze.+Ndipo andimenya mbama pofuna kundichititsa manyazi.Iwo asonkhana ambirimbiri kuti alimbane nane.+ Yobu 16:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Anzanga akundinyoza+Pamene ndikupemphera kwa Mulungu ndikugwetsa misozi.+ Yobu 17:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Anthu onyoza andizungulira,+Ndipo diso langa likuyenera kuyangʼanitsitsa* khalidwe lawo lopanduka. Aheberi 11:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Ena anakumana ndi mayesero chifukwa ananyozedwa komanso kukwapulidwa. Kuwonjezera pamenepo anamangidwa+ ndiponso kutsekeredwa mʼndende.+
10 Anthu atsegula kukamwa kwawo kuti andimeze.+Ndipo andimenya mbama pofuna kundichititsa manyazi.Iwo asonkhana ambirimbiri kuti alimbane nane.+
36 Ena anakumana ndi mayesero chifukwa ananyozedwa komanso kukwapulidwa. Kuwonjezera pamenepo anamangidwa+ ndiponso kutsekeredwa mʼndende.+