Salimo 73:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Chifukwa ndinkachitira nsanje anthu onyada*Ndikamaona mtendere wa anthu oipa.+ Salimo 73:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Iwo savutika ngati mmene anthu ena amavutikira,+Ndipo sakumana ndi mavuto mofanana ndi anthu ena.+