Yobu 12:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Anthu akuba amakhala mwamtendere mʼmatenti awo,+Amene amakwiyitsa Mulungu amakhala otetezeka,+Anthu amene mulungu wawo ali mʼmanja mwawo. Yobu 21:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Nʼchifukwa chiyani oipa amakhalabe ndi moyo,+Amakalamba komanso amalemera* kwambiri?+ Yobu 21:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Nyumba zawo nʼzotetezeka ndipo saopa chilichonse,+Mulungu sawalanga ndi ndodo yake.
6 Anthu akuba amakhala mwamtendere mʼmatenti awo,+Amene amakwiyitsa Mulungu amakhala otetezeka,+Anthu amene mulungu wawo ali mʼmanja mwawo.