2 Samueli 12:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Nʼchifukwa chiyani unanyoza mawu a Yehova pochita zoipa pamaso pake? Unapha Uriya Muhiti ndi lupanga.+ Kenako unatenga mkazi wake kuti akhale mkazi wako+ utapha Uriyayo ndi lupanga la Aamoni.+ 2 Samueli 12:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Iweyo unachita zimenezi mobisa,+ koma ine ndidzazichita masana Aisiraeli onse akuona.’” Salimo 94:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Inu Yehova, kodi anthu oipa adzapitiriza kusangalala mpaka liti?Adzapitiriza kukondwera mpaka liti?+ Salimo 94:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Iwo amanena kuti: “Ya sakuona,+Ndipo Mulungu wa Yakobo sakudziwa zimene zikuchitika.”+ Miyambo 30:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Zimene mkazi wachigololo amachita ndi izi: Iye amadya nʼkupukuta pakamwa pakeKenako amanena kuti, “Sindinachite cholakwa chilichonse.”+
9 Nʼchifukwa chiyani unanyoza mawu a Yehova pochita zoipa pamaso pake? Unapha Uriya Muhiti ndi lupanga.+ Kenako unatenga mkazi wake kuti akhale mkazi wako+ utapha Uriyayo ndi lupanga la Aamoni.+
3 Inu Yehova, kodi anthu oipa adzapitiriza kusangalala mpaka liti?Adzapitiriza kukondwera mpaka liti?+
20 Zimene mkazi wachigololo amachita ndi izi: Iye amadya nʼkupukuta pakamwa pakeKenako amanena kuti, “Sindinachite cholakwa chilichonse.”+