Salimo 10:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Chifukwa cha kudzikweza, munthu woipa safufuza kuti adziwe Mulungu.Iye amangoganiza kuti: “Kulibe Mulungu.”+ Salimo 10:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Mumtima mwake amanena kuti: “Mulungu waiwala zoipa zimene ndimachita.+ Iye wayangʼana kumbali. Sakuona chilichonse.”+ Salimo 73:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Chifukwa ndinkachitira nsanje anthu onyada*Ndikamaona mtendere wa anthu oipa.+ Salimo 73:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Iwo amanena kuti: “Mulungu angadziwe bwanji?+ Kodi Wamʼmwambamwamba amadziwa chilichonse?” Yesaya 29:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Tsoka kwa anthu amene amayesa kubisira Yehova mapulani awo oipa.*+ Zochita zawo amazichitira mumdima,Ndipo amati: “Ndi ndani akutiona? Ndi ndani akudziwa zimene tikuchita?”+
4 Chifukwa cha kudzikweza, munthu woipa safufuza kuti adziwe Mulungu.Iye amangoganiza kuti: “Kulibe Mulungu.”+
11 Mumtima mwake amanena kuti: “Mulungu waiwala zoipa zimene ndimachita.+ Iye wayangʼana kumbali. Sakuona chilichonse.”+
15 Tsoka kwa anthu amene amayesa kubisira Yehova mapulani awo oipa.*+ Zochita zawo amazichitira mumdima,Ndipo amati: “Ndi ndani akutiona? Ndi ndani akudziwa zimene tikuchita?”+