Miyambo 15:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Yehova ali kutali ndi anthu oipa,Koma amamva pemphero la anthu olungama.+ Yesaya 1:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Ndipo mukatambasula manja anu,Ndimakubisirani maso anga.+ Ngakhale mupereke mapemphero ambiri,+Ine sindimvetsera.+Manja anu adzaza magazi.+ Yeremiya 11:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Choncho Yehova wanena kuti, ‘Ndiwagwetsera tsoka+ limene sadzatha kulithawa. Akadzandiitana kuti ndiwathandize, sindidzawamvetsera.+
15 Ndipo mukatambasula manja anu,Ndimakubisirani maso anga.+ Ngakhale mupereke mapemphero ambiri,+Ine sindimvetsera.+Manja anu adzaza magazi.+
11 Choncho Yehova wanena kuti, ‘Ndiwagwetsera tsoka+ limene sadzatha kulithawa. Akadzandiitana kuti ndiwathandize, sindidzawamvetsera.+