Miyambo 19:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Munthu wosachedwa kupsa mtima ayenera kulipira,Chifukwa ukayesa kumʼpulumutsa, uzichita zimenezi kawirikawiri.+ Miyambo 29:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Munthu wosachedwa kukwiya amayambitsa mkangano.+Aliyense amene sachedwa kupsa mtima amakhala ndi machimo ambiri.+
19 Munthu wosachedwa kupsa mtima ayenera kulipira,Chifukwa ukayesa kumʼpulumutsa, uzichita zimenezi kawirikawiri.+
22 Munthu wosachedwa kukwiya amayambitsa mkangano.+Aliyense amene sachedwa kupsa mtima amakhala ndi machimo ambiri.+