Aheberi 11:24, 25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Chifukwa cha chikhulupiriro, Mose atakula+ anakana kutchedwa mwana wa mwana wamkazi wa Farao,+ 25 ndipo anasankha kuzunzidwa limodzi ndi anthu a Mulungu, mʼmalo mochita machimo nʼkusangalala kwa nthawi yochepa.
24 Chifukwa cha chikhulupiriro, Mose atakula+ anakana kutchedwa mwana wa mwana wamkazi wa Farao,+ 25 ndipo anasankha kuzunzidwa limodzi ndi anthu a Mulungu, mʼmalo mochita machimo nʼkusangalala kwa nthawi yochepa.