-
Aheberi 11:25Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
25 ndipo anasankha kuzunzidwa pamodzi ndi anthu a Mulungu, m’malo mochita zinthu zosangalatsa koma zosakhalitsa zauchimo.
-