-
Aheberi 11:25Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
25 ndipo anasankha kuzunzidwa limodzi ndi anthu a Mulungu, mʼmalo mochita machimo nʼkusangalala kwa nthawi yochepa.
-