Salimo 104:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Mulungu amathirira mapiri kuchokera mʼzipinda zake zamʼmwamba.+ Dziko lapansi ladzaza ndi zipatso za ntchito zanu.+ Salimo 107:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Chipululu amachisandutsa dambo la madzi,Ndipo dziko louma amalisandutsa dera la akasupe amadzi.+
13 Mulungu amathirira mapiri kuchokera mʼzipinda zake zamʼmwamba.+ Dziko lapansi ladzaza ndi zipatso za ntchito zanu.+