Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Mateyu 27:1, 2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 27 Mʼmawa kutacha, ansembe aakulu onse limodzi ndi akulu a anthu anakambirana nʼkugwirizana kuti aphe Yesu.+ 2 Ndipo atamumanga, anapita kukamupereka kwa Bwanamkubwa Pilato.+

  • Luka 23:10, 11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Komabe ansembe aakulu ndi alembi ankangonyamukanyamuka nʼkumamuneneza mwaukali. 11 Ndiyeno Herode limodzi ndi asilikali ake anamuchitira zachipongwe.+ Anamunyoza+ pomuveka chovala chokongola kwambiri, kenako anamutumizanso kwa Pilato.

  • Chivumbulutso 19:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Ndiyeno ndinaona chilombo, mafumu a dziko lapansi ndi asilikali awo atasonkhana pamodzi kuti amenyane ndi amene anakwera pahatchi uja ndi gulu lake lankhondo.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena