Chivumbulutso 16:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Kwenikweni amenewa ndi mauthenga ouziridwa ndi ziwanda ndipo amachita zizindikiro.+ Mauthengawo akupita kwa mafumu a dziko lonse lapansi kumene kuli anthu, kuti awasonkhanitse pamodzi kunkhondo+ ya tsiku lalikulu la Mulungu Wamphamvuyonse.+ Chivumbulutso 16:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Ndipo anawasonkhanitsa pamodzi, kumalo amene mʼChiheberi amatchulidwa kuti Aramagedo.*+
14 Kwenikweni amenewa ndi mauthenga ouziridwa ndi ziwanda ndipo amachita zizindikiro.+ Mauthengawo akupita kwa mafumu a dziko lonse lapansi kumene kuli anthu, kuti awasonkhanitse pamodzi kunkhondo+ ya tsiku lalikulu la Mulungu Wamphamvuyonse.+