Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 2 Mbiri 35:22
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 Koma Yosiya anadzisintha+ nʼkupitabe kukamenyana naye. Iye sanamvere mawu a Neko omwe anali ochokera kwa Mulungu. Choncho anapita kukamenyana naye mʼchigwa cha Megido.+

  • Zekariya 12:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Pa tsiku limenelo, anthu adzalira kwambiri mu Yerusalemu ngati mmene analirira ku Hadadirimoni, mʼchigwa cha Megido.+

  • Chivumbulutso 19:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Ndiyeno ndinaona chilombo, mafumu a dziko lapansi ndi asilikali awo atasonkhana pamodzi kuti amenyane ndi amene anakwera pahatchi uja ndi gulu lake lankhondo.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena