Salimo 27:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Yembekezera Yehova.+Limba mtima ndipo uchite zinthu mwamphamvu.+ Inde, yembekezera Yehova. Salimo 123:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Mofanana ndi mmene maso a atumiki amayangʼanira dzanja la mbuye wawo,Komanso mmene maso a kapolo wamkazi amayangʼanira dzanja la mbuye wake wamkazi,Maso athu akuyangʼana kwa Yehova Mulungu wathu,+Mpakana atatikomera mtima.+ Miyambo 18:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Dzina la Yehova ndi nsanja yolimba.+ Wolungama amathawira mmenemo ndipo amatetezedwa.*+
2 Mofanana ndi mmene maso a atumiki amayangʼanira dzanja la mbuye wawo,Komanso mmene maso a kapolo wamkazi amayangʼanira dzanja la mbuye wake wamkazi,Maso athu akuyangʼana kwa Yehova Mulungu wathu,+Mpakana atatikomera mtima.+