Salimo 123:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Taonani! Monga mmene maso a atumiki amayang’anira dzanja la mbuye wawo,+Mmene maso a kapolo wamkazi amayang’anira dzanja la mbuye wake wamkazi,+Momwemonso, maso athu adzayang’ana kwa Yehova Mulungu wathu,+Kufikira atatikomera mtima.+ Masalimo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 123:2 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),7/2018, ptsa. 12-13 Nsanja ya Olonda,9/1/2006, tsa. 15
2 Taonani! Monga mmene maso a atumiki amayang’anira dzanja la mbuye wawo,+Mmene maso a kapolo wamkazi amayang’anira dzanja la mbuye wake wamkazi,+Momwemonso, maso athu adzayang’ana kwa Yehova Mulungu wathu,+Kufikira atatikomera mtima.+