Salimo 123:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Mofanana ndi mmene maso a atumiki amayangʼanira dzanja la mbuye wawo,Komanso mmene maso a kapolo wamkazi amayangʼanira dzanja la mbuye wake wamkazi,Maso athu akuyangʼana kwa Yehova Mulungu wathu,+Mpakana atatikomera mtima.+ Masalimo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 123:2 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),7/2018, ptsa. 12-13 Nsanja ya Olonda,9/1/2006, tsa. 15
2 Mofanana ndi mmene maso a atumiki amayangʼanira dzanja la mbuye wawo,Komanso mmene maso a kapolo wamkazi amayangʼanira dzanja la mbuye wake wamkazi,Maso athu akuyangʼana kwa Yehova Mulungu wathu,+Mpakana atatikomera mtima.+