Salimo 22:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Iwo atsegula pakamwa pawo nʼkumandiopseza,+Ngati mkango wobangula umene umakhadzulakhadzula nyama.+ Salimo 35:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Inu Yehova, kodi mudzayangʼanira zimenezi mpaka liti?+ Ndipulumutseni kuti asandiphe,+Pulumutsani moyo wanga,* womwe ndi wamtengo wapatali, kwa mikango yamphamvu.*+
13 Iwo atsegula pakamwa pawo nʼkumandiopseza,+Ngati mkango wobangula umene umakhadzulakhadzula nyama.+
17 Inu Yehova, kodi mudzayangʼanira zimenezi mpaka liti?+ Ndipulumutseni kuti asandiphe,+Pulumutsani moyo wanga,* womwe ndi wamtengo wapatali, kwa mikango yamphamvu.*+