Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 52:5, 6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  5 Nʼchifukwa chake Mulungu adzakugwetsa ndipo sudzakhalakonso.+

      Adzakugwira nʼkukukokera kutali ndi tenti yako,+

      Ndipo adzakuzula nʼkukuchotsa mʼdziko la anthu amoyo.+ (Selah)

       6 Olungama adzaona zimenezi nʼkuchita mantha,+

      Ndipo adzamuseka+ kuti:

  • Salimo 64:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Wolungama adzasangalala chifukwa cha Yehova ndipo adzathawira kwa iye.+

      Onse owongoka mtima adzasangalala kwambiri.*

  • Ezekieli 25:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Anthu amenewa ndidzawachitira zinthu zopweteka powabwezera ndipo ndidzawalanga mwaukali. Ndikadzawalanga, adzadziwa kuti ine ndine Yehova.”’”

  • Chivumbulutso 18:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 Sangalalani kumwambako chifukwa cha zimene zamuchitikira.+ Inunso oyera,+ atumwi ndi aneneri, sangalalani chifukwa Mulungu wamupatsa chilango chifukwa cha zomwe anakuchitirani.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena