Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 18:35
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 35 Inu mumandipatsa chishango chanu chachipulumutso,+

      Dzanja lanu lamanja limandithandiza,*

      Ndipo kudzichepetsa kwanu nʼkumene kumandikweza.+

  • Salimo 21:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  8 Dzanja lanu lidzapeza adani anu onse.

      Dzanja lanu lamanja lidzapeza anthu amene amadana nanu.

  • Salimo 108:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  6 Kuti anthu amene mumawakonda apulumutsidwe,

      Tipulumutseni ndi dzanja lanu lamanja ndipo mundiyankhe.+

  • Salimo 118:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Phokoso lachisangalalo komanso chipulumutso*

      Likumveka mʼmatenti a anthu olungama.

      Dzanja lamanja la Yehova likusonyeza mphamvu zake.+

  • Yesaya 41:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Usachite mantha, chifukwa ndili ndi iwe.+

      Usade nkhawa chifukwa ine ndine Mulungu wako.+

      Ndikulimbitsa, ndithu ndikuthandiza,+

      Ndikugwira mwamphamvu ndi dzanja langa lamanja lachilungamo.’

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena