Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 30:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  5 Chifukwa mkwiyo wa Mulungu sukhalitsa pa munthu,+

      Koma munthu amene wasangalala naye* amamukomera mtima kwa moyo wake wonse.+

      Munthu akhoza kulira usiku, koma mʼmawa amafuula mosangalala.+

  • Salimo 100:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  5 Chifukwa Yehova ndi wabwino.+

      Chikondi chake chokhulupirika chidzakhalapo mpaka kalekale,

      Ndipo kukhulupirika kwake kudzakhalapo ku mibadwo yonse.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena