Salimo 10:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Chifukwa cha kudzikweza, munthu woipa safufuza kuti adziwe Mulungu.Iye amangoganiza kuti: “Kulibe Mulungu.”+ Salimo 10:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Mumtima mwake amanena kuti: “Mulungu waiwala zoipa zimene ndimachita.+ Iye wayangʼana kumbali. Sakuona chilichonse.”+ Salimo 59:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Tamverani zimene zikutuluka pakamwa pawo.Milomo yawo ili ngati malupanga,+Chifukwa iwo akuti: “Ndani akumvetsera?”+
4 Chifukwa cha kudzikweza, munthu woipa safufuza kuti adziwe Mulungu.Iye amangoganiza kuti: “Kulibe Mulungu.”+
11 Mumtima mwake amanena kuti: “Mulungu waiwala zoipa zimene ndimachita.+ Iye wayangʼana kumbali. Sakuona chilichonse.”+
7 Tamverani zimene zikutuluka pakamwa pawo.Milomo yawo ili ngati malupanga,+Chifukwa iwo akuti: “Ndani akumvetsera?”+