Salimo 56:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Inu Mulungu, ine ndikuyenera kukwaniritsa zimene ndinakulonjezani.+Ndidzapereka kwa inu nsembe zoyamikira.+ Salimo 116:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Ndidzakwaniritsa malonjezo anga kwa Yehova,Pamaso pa anthu ake onse.+ Mlaliki 5:4, 5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ukalonjeza kwa Mulungu usamachedwe kukwaniritsa lonjezo lako,+ chifukwa Mulungu sasangalala ndi anthu opusa.+ Uzikwaniritsa zinthu zimene walonjeza.+ 5 Ndi bwino kuti usalonjeze kusiyana ndi kulonjeza koma osakwaniritsa zimene walonjezazo.+
12 Inu Mulungu, ine ndikuyenera kukwaniritsa zimene ndinakulonjezani.+Ndidzapereka kwa inu nsembe zoyamikira.+
4 Ukalonjeza kwa Mulungu usamachedwe kukwaniritsa lonjezo lako,+ chifukwa Mulungu sasangalala ndi anthu opusa.+ Uzikwaniritsa zinthu zimene walonjeza.+ 5 Ndi bwino kuti usalonjeze kusiyana ndi kulonjeza koma osakwaniritsa zimene walonjezazo.+