-
Mateyu 27:29Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
29 Komanso analuka chisoti chachifumu chaminga nʼkumuveka kumutu ndipo anamupatsa bango mʼdzanja lake lamanja. Kenako anamugwadira nʼkumamunyoza kuti: “Moni, inu Mfumu ya Ayuda!”
-