Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 3:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  2 Anthu ambiri akunena za ine* kuti:

      “Mulungu samupulumutsa ameneyu.”+ (Selah)*

  • Salimo 42:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Anthu amene amadana nane kwambiri akundinyoza,*

      Amandinyoza tsiku lonse kuti: “Mulungu wako ali kuti?”+

  • Mateyu 27:42, 43
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 42 “Ena anatha kuwapulumutsa, koma kuti adzipulumutse yekha zikumukanika! Ngati ali Mfumu ya Isiraeli,+ tiyeni tione ngati angatsike pamtengo wozunzikirapowo* ndipo ife timukhulupirira. 43 Paja iye amakhulupirira Mulungu, ndiye panopa Mulunguyo amupulumutse ngati akumufunadi+ chifukwa iye ankanena kuti, ‘Ine ndine Mwana wa Mulungu.’”+

Mabuku a Chichewa (1974-2026)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena