2 Mbiri 32:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Zimenezi zitachitika, anthu ambiri ankabweretsa mphatso kwa Yehova ku Yerusalemu ndi zinthu zabwino kwambiri kwa Hezekiya mfumu ya Yuda,+ moti iye ankalemekezedwa ndi anthu a mitundu yonse. Salimo 89:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Mulungu ndi wochititsa mantha komanso wolemekezeka pakati pa gulu lake la oyera.*+Iye ndi wamkulu komanso wochititsa mantha kwa onse amene amuzungulira.+
23 Zimenezi zitachitika, anthu ambiri ankabweretsa mphatso kwa Yehova ku Yerusalemu ndi zinthu zabwino kwambiri kwa Hezekiya mfumu ya Yuda,+ moti iye ankalemekezedwa ndi anthu a mitundu yonse.
7 Mulungu ndi wochititsa mantha komanso wolemekezeka pakati pa gulu lake la oyera.*+Iye ndi wamkulu komanso wochititsa mantha kwa onse amene amuzungulira.+