Salimo 79:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Inu Yehova, kodi mukhala wokwiya mpaka liti? Kwamuyaya?+ Kodi mkwiyo wanu ukhala ukuyaka ngati moto mpaka liti?+
5 Inu Yehova, kodi mukhala wokwiya mpaka liti? Kwamuyaya?+ Kodi mkwiyo wanu ukhala ukuyaka ngati moto mpaka liti?+