-
Ekisodo 17:6, 7Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
6 Tamvera! Ine ndidzatsogola nʼkukaima pathanthwe ku Horebe. Kumeneko ukamenye thanthwelo ndipo padzatuluka madzi amene anthu adzamwe.”+ Mose anachitadi zomwezo pamaso pa akulu a Isiraeli. 7 Choncho iye anatchula malowo kuti Masa*+ ndi Meriba,*+ chifukwa Aisiraeli anakangana ndi Mose komanso chifukwa chakuti anayesa Yehova+ kuti: “Kodi pakati pathu pano, Yehova alipo kapena ayi?”
-