Ekisodo 6:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Ndinkaonekera kwa Abulahamu, Isaki ndi Yakobo monga Mulungu Wamphamvuyonse.+ Koma za dzina langa lakuti Yehova,+ ine sindinadzidziwikitse kwa iwo.+ Salimo 68:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Imbirani Mulungu, muimbireni nyimbo zotamanda dzina lake.+ Imbirani Iye amene akudutsa mʼchipululu.* Dzina lake ndi Ya.*+ Sangalalani pamaso pake. Yesaya 42:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ine ndine Yehova. Dzina langa ndi limeneli.Sindipereka ulemerero wanga kwa wina aliyenseNdipo sindifuna kuti aliyense azitamanda zifaniziro zogoba mʼmalo mwa ine.+ Yesaya 54:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Chifukwa Wokupanga Wamkulu+ ali ngati mwamuna* wako,+Dzina lake ndi Yehova wa magulu ankhondo akumwamba,Ndipo Woyera wa Isiraeli ndiye Wokuwombola.+ Iye adzatchedwa Mulungu wa dziko lonse lapansi.+
3 Ndinkaonekera kwa Abulahamu, Isaki ndi Yakobo monga Mulungu Wamphamvuyonse.+ Koma za dzina langa lakuti Yehova,+ ine sindinadzidziwikitse kwa iwo.+
4 Imbirani Mulungu, muimbireni nyimbo zotamanda dzina lake.+ Imbirani Iye amene akudutsa mʼchipululu.* Dzina lake ndi Ya.*+ Sangalalani pamaso pake.
8 Ine ndine Yehova. Dzina langa ndi limeneli.Sindipereka ulemerero wanga kwa wina aliyenseNdipo sindifuna kuti aliyense azitamanda zifaniziro zogoba mʼmalo mwa ine.+
5 Chifukwa Wokupanga Wamkulu+ ali ngati mwamuna* wako,+Dzina lake ndi Yehova wa magulu ankhondo akumwamba,Ndipo Woyera wa Isiraeli ndiye Wokuwombola.+ Iye adzatchedwa Mulungu wa dziko lonse lapansi.+