Zekariya 14:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Yehova adzakhala Mfumu ya dziko lonse lapansi.+ Pa tsiku limenelo, Yehova adzakhala mmodzi+ ndipo dzina lake lidzakhala limodzi.+ Aroma 3:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Kapena kodi iye ndi Mulungu wa Ayuda okha?+ Kodi si Mulungu wa anthu a mitundu inanso?+ Inde, iye ndi Mulungunso wa anthu a mitundu ina.+
9 Yehova adzakhala Mfumu ya dziko lonse lapansi.+ Pa tsiku limenelo, Yehova adzakhala mmodzi+ ndipo dzina lake lidzakhala limodzi.+
29 Kapena kodi iye ndi Mulungu wa Ayuda okha?+ Kodi si Mulungu wa anthu a mitundu inanso?+ Inde, iye ndi Mulungunso wa anthu a mitundu ina.+