Aroma 3:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Kapena kodi iye ndi Mulungu wa Ayuda okha?+ Kodi salinso Mulungu wa anthu a mitundu ina?+ Inde, iye alinso Mulungu wa anthu a mitundu ina,+ Aroma Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 3:29 Galamukani!,5/8/2001, ptsa. 28-29
29 Kapena kodi iye ndi Mulungu wa Ayuda okha?+ Kodi salinso Mulungu wa anthu a mitundu ina?+ Inde, iye alinso Mulungu wa anthu a mitundu ina,+