Yesaya 54:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 “Pakuti Wokupanga Wamkulu+ ndiye mwamuna wako.+ Dzina lake ndi Yehova wa makamu,+ ndipo Woyera wa Isiraeli ndiye Wokuwombola.+ Iye adzatchedwa Mulungu wa dziko lonse lapansi.+ Aroma 10:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Palibe kusiyana pakati pa Myuda ndi Mgiriki,+ popeza kwa onsewo Ambuye ndi mmodzi, amene amapereka mowolowa manja+ kwa onse oitana pa dzina lake. Agalatiya 3:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Cholinga chake chinali chakuti mitundu ipeze madalitso amene Abulahamu analonjezedwa kudzera mwa Yesu Khristu,+ kuti tidzalandire mzimu wolonjezedwawo+ chifukwa cha chikhulupiriro chathu.+
5 “Pakuti Wokupanga Wamkulu+ ndiye mwamuna wako.+ Dzina lake ndi Yehova wa makamu,+ ndipo Woyera wa Isiraeli ndiye Wokuwombola.+ Iye adzatchedwa Mulungu wa dziko lonse lapansi.+
12 Palibe kusiyana pakati pa Myuda ndi Mgiriki,+ popeza kwa onsewo Ambuye ndi mmodzi, amene amapereka mowolowa manja+ kwa onse oitana pa dzina lake.
14 Cholinga chake chinali chakuti mitundu ipeze madalitso amene Abulahamu analonjezedwa kudzera mwa Yesu Khristu,+ kuti tidzalandire mzimu wolonjezedwawo+ chifukwa cha chikhulupiriro chathu.+