Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 18:32
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 32 Mulungu woona ndi amene amandipatsa mphamvu,+

      Ndipo adzasalaza njira yanga.+

  • Yesaya 40:29-31
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 29 Iye amapereka mphamvu kwa munthu wotopa

      Ndipo munthu amene alibe mphamvu amamupatsa mphamvu zambiri.+

      30 Anyamata adzatopa nʼkufooka,

      Ndipo amuna achinyamata adzapunthwa nʼkugwa,

      31 Koma anthu amene amayembekezera Yehova adzapezanso mphamvu.

      Iwo adzaulukira mʼmwamba ngati kuti ali ndi mapiko a chiwombankhanga.+

      Adzathamanga koma osafooka.

      Adzayenda koma osatopa.”+

  • Habakuku 3:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, ndi amene amandipatsa mphamvu.+

      Iye adzachititsa kuti miyendo yanga ikhale ngati ya mbawala,

      Komanso kuti ndiponde pamalo okwera.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena