Yeremiya 50:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 “Mʼmasiku amenewo ndiponso pa nthawi imeneyo,Cholakwa cha Isiraeli chidzafufuzidwa,Koma sichidzapezeka,” akutero Yehova.“Machimo a Yuda sadzapezeka,Chifukwa ine ndidzakhululukira anthu amene ndidzawasiye ndi moyo.”+ Mika 7:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Kodi pali Mulungu winanso wofanana ndi inu,Amene amakhululukira zolakwa ndi machimo+ a anthu ake otsala omwe ndi cholowa chake?+ Inu simudzakhalabe wokwiya mpaka kalekale,Chifukwa mumakonda chikondi chokhulupirika.+
20 “Mʼmasiku amenewo ndiponso pa nthawi imeneyo,Cholakwa cha Isiraeli chidzafufuzidwa,Koma sichidzapezeka,” akutero Yehova.“Machimo a Yuda sadzapezeka,Chifukwa ine ndidzakhululukira anthu amene ndidzawasiye ndi moyo.”+
18 Kodi pali Mulungu winanso wofanana ndi inu,Amene amakhululukira zolakwa ndi machimo+ a anthu ake otsala omwe ndi cholowa chake?+ Inu simudzakhalabe wokwiya mpaka kalekale,Chifukwa mumakonda chikondi chokhulupirika.+