1 Mbiri 16:41 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 41 Iwowa anali limodzi ndi Hemani ndi Yedutuni+ ndiponso amuna onse amene anawasankha mochita kuwatchula mayina kuti azithokoza Yehova,+ chifukwa “chikondi chake chokhulupirika chidzakhalapo mpaka kalekale.”+ Yesaya 54:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Mapiri akhoza kuchotsedwa,Ndipo zitunda zikhoza kugwedezeka,Koma chikondi changa chokhulupirika sichidzachotsedwa pa iwe,+Ndipo pangano langa lamtendere silidzagwedezeka,”+ akutero Yehova, amene akukuchitira chifundo.+
41 Iwowa anali limodzi ndi Hemani ndi Yedutuni+ ndiponso amuna onse amene anawasankha mochita kuwatchula mayina kuti azithokoza Yehova,+ chifukwa “chikondi chake chokhulupirika chidzakhalapo mpaka kalekale.”+
10 Mapiri akhoza kuchotsedwa,Ndipo zitunda zikhoza kugwedezeka,Koma chikondi changa chokhulupirika sichidzachotsedwa pa iwe,+Ndipo pangano langa lamtendere silidzagwedezeka,”+ akutero Yehova, amene akukuchitira chifundo.+