Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 19:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  7 Chilamulo cha Yehova ndi changwiro,+ chimabwezeretsa mphamvu.*+

      Zikumbutso za Yehova ndi zodalirika,+ zimapatsa nzeru munthu wosadziwa zinthu.+

  • Salimo 40:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  8 Ndimasangalala* kuchita zimene mumafuna, inu Mulungu wanga,+

      Ndipo chilamulo chanu chili mumtima mwanga.+

  • Salimo 112:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 112 Tamandani Ya!*+

      א [Aleph]

      Wosangalala ndi munthu amene amaopa Yehova,+

      ב [Beth]

      Amene amasangalala kwambiri ndi malamulo ake.+

  • Mateyu 5:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 “Osangalala ndi anthu amene amazindikira zosowa zawo zauzimu+ chifukwa Ufumu wakumwamba ndi wawo.

  • Aroma 7:22
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 Mumtima mwanga ndimasangalala kwambiri ndi malamulo a Mulungu,+

  • Yakobo 1:25
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 25 Koma amene amayangʼanitsitsa mulamulo langwiro+ limene limabweretsa ufulu ndipo amapitiriza kuliyangʼanitsitsa, adzakhala wosangalala ndi zimene akuchita+ chifukwa chakuti si munthu amene amangomva nʼkuiwala, koma amene amachita zimene wamvazo.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena