Salimo 50:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Amene akundiyamikira kuti ikhale nsembe imene akupereka kwa ine akundilemekeza.+Ndipo munthu amene akupitiriza kuchita zabwino,Ndidzamuonetsa chipulumutso changa.”+ Salimo 66:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Ndidzalowa mʼnyumba yanu ndi nsembe zopsereza zathunthu.+Ine ndidzakwaniritsa malonjezo anga kwa inu+ Salimo 122:1, 2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 122 Ndinasangalala pamene anandiuza kuti: “Tiyeni tipite kunyumba ya Yehova.”+ 2 Ndipo tsopano mapazi athu aimaPamageti ako iwe Yerusalemu.+
23 Amene akundiyamikira kuti ikhale nsembe imene akupereka kwa ine akundilemekeza.+Ndipo munthu amene akupitiriza kuchita zabwino,Ndidzamuonetsa chipulumutso changa.”+
13 Ndidzalowa mʼnyumba yanu ndi nsembe zopsereza zathunthu.+Ine ndidzakwaniritsa malonjezo anga kwa inu+ Salimo 122:1, 2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 122 Ndinasangalala pamene anandiuza kuti: “Tiyeni tipite kunyumba ya Yehova.”+ 2 Ndipo tsopano mapazi athu aimaPamageti ako iwe Yerusalemu.+
122 Ndinasangalala pamene anandiuza kuti: “Tiyeni tipite kunyumba ya Yehova.”+ 2 Ndipo tsopano mapazi athu aimaPamageti ako iwe Yerusalemu.+