Salimo 55:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 55 Inu Mulungu, mvetserani pemphero langa,+Ndipo musanyalanyaze pempho langa lakuti mundichitire chifundo.*+ Danieli 9:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Tsopano inu Mulungu wathu, imvani pemphero langa ine mtumiki wanu ndi kuchonderera kwanga. Malo anu opatulika+ amene awonongedwa+ akomereni mtima, inu Yehova, chifukwa cha dzina lanu.
55 Inu Mulungu, mvetserani pemphero langa,+Ndipo musanyalanyaze pempho langa lakuti mundichitire chifundo.*+
17 Tsopano inu Mulungu wathu, imvani pemphero langa ine mtumiki wanu ndi kuchonderera kwanga. Malo anu opatulika+ amene awonongedwa+ akomereni mtima, inu Yehova, chifukwa cha dzina lanu.