-
Salimo 8:3Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
3 Ndikayangʼana kumwamba, ntchito ya zala zanu,
Mwezi ndi nyenyezi zimene munapanga,+
-
Aheberi 1:10-12Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
10 Iye akunenanso kuti: “Ambuye, pachiyambipo munakhazikitsa maziko a dziko lapansi, ndipo kumwamba ndi ntchito ya manja anu. 11 Zinthu zimenezi zidzatha, koma inu mudzakhalapobe. Mofanana ndi chovala, zonsezi zidzatha. 12 Mudzapindapinda zinthu zimenezi ngati mkanjo komanso ngati chovala ndipo zidzasinthidwa. Koma inu simudzasintha, ndipo mudzakhalapo mpaka kalekale.”+
-
-
-