Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 19:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Zinthu zakumwamba zikulengeza ulemerero wa Mulungu.+

      Ndipo mumlengalenga mukufotokoza ntchito ya manja ake.+

  • Salimo 104:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Wapanga mwezi kuti uzisonyeza nthawi yoikidwiratu.

      Dzuwa limadziwa bwino nthawi yoyenera kulowa.+

  • Yesaya 40:26
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 26 “Kwezani maso anu kumwamba ndipo muone.

      Kodi ndi ndani amene analenga zinthu zimenezi?+

      Ndi amene akutsogolera gulu lonse la nyenyezi ndipo zonse amaziwerenga.

      Iliyonse amaiitana poitchula dzina lake.+

      Chifukwa cha kuchuluka kwa mphamvu zake zoopsa ndiponso chifukwa chakuti ali ndi mphamvu zambiri zochitira zinthu,+

      Palibe iliyonse imene imasowa.

  • Aroma 1:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 Kuchokera pamene dziko linalengedwa, makhalidwe a Mulungu osaoneka ndi maso akuonekera bwino. Makhalidwe a Mulungu amenewa,+ ngakhalenso mphamvu zake zosatha+ ndiponso Umulungu wake,+ zikuonekera mʼzinthu zimene anapanga moti anthuwo alibenso chifukwa chomveka chosakhulupirira kuti kuli Mulungu.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena