Salimo 104:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Wapanga mwezi kuti uzisonyeza nthawi yoikidwiratu.+Dzuwa nalo limadziwa bwino kumene limalowera.+