Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 15:26
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 26 Iye anawauza kuti: “Mukadzamvera ndi mtima wonse mawu a Yehova Mulungu wanu, nʼkuchita zinthu zoyenera pamaso pake ndiponso kumvera malamulo ake ndi kusunga malangizo ake onse,+ sindidzakugwetserani matenda aliwonse amene ndinagwetsera Aiguputo,+ chifukwa ine Yehova ndi amene ndikukuchiritsani.”+

  • Salimo 41:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  3 Yehova adzathandiza munthu woganizira wonyozekayo pamene akudwala pabedi lake.+

      Mudzamusamalira bwino kwambiri pa nthawi imene akudwala.

  • Salimo 147:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  3 Iye amachiritsa anthu osweka mtima,

      Ndipo amamanga mabala awo.

  • Yesaya 33:24
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 24 Ndipo palibe munthu wokhala mʼdzikolo amene adzanene kuti: “Ine ndikudwala.”+

      Anthu okhala mʼdzikolo adzakhululukidwa machimo awo.+

  • Yakobo 5:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Pemphero lachikhulupiriro lidzachiritsa munthu amene akudwalayo* ndipo Yehova* adzamulimbitsa. Komanso ngati anachita machimo, adzakhululukidwa.

  • Chivumbulutso 21:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Iye adzapukuta misozi yonse mʼmaso mwawo+ ndipo imfa sidzakhalaponso.+ Sipadzakhalanso kulira, kubuula kapena kupweteka.+ Zakalezo zapita.”

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena