Miyambo 12:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Njira yachilungamo imathandiza munthu kuti akhale ndi moyo,+Ndipo mʼnjira yake mulibe imfa.