Ezekieli 1:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Angelowo ankaoneka ngati makala oyaka moto. Pakati pa angelowo panali zinazake zooneka ngati miyuni ya moto wowala imene inkayenda kuchokera kwa mngelo wina kupita kwa mngelo wina ndipo mʼmotowo munkatuluka mphezi.+ Aheberi 1:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ndiponso ponena za angelo, iye akuti: “Amachititsa kuti angelo ake akhale amphamvu* ndipo amachititsa atumiki ake+ kukhala ngati lawi la moto.”+ Aheberi 1:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Angelo onse ndi mizimu yotumikira ena.*+ Mulungu amawatumiza kuti akatumikire omwe iye adzawapulumutse.
13 Angelowo ankaoneka ngati makala oyaka moto. Pakati pa angelowo panali zinazake zooneka ngati miyuni ya moto wowala imene inkayenda kuchokera kwa mngelo wina kupita kwa mngelo wina ndipo mʼmotowo munkatuluka mphezi.+
7 Ndiponso ponena za angelo, iye akuti: “Amachititsa kuti angelo ake akhale amphamvu* ndipo amachititsa atumiki ake+ kukhala ngati lawi la moto.”+
14 Angelo onse ndi mizimu yotumikira ena.*+ Mulungu amawatumiza kuti akatumikire omwe iye adzawapulumutse.