Salimo 107:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Chifukwa iye wathetsa ludzu la anthu aludzuNdipo anthu anjala wawadyetsa zinthu zabwino.+ Salimo 145:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Mumatambasula dzanja lanuNʼkukwaniritsa zolakalaka za chamoyo chilichonse.+