Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 41:39-41
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 39 Kenako Farao anauza Yosefe kuti: “Popeza kuti Mulungu wakudziwitsa zonsezi, palibenso munthu wina wozindikira ndi wanzeru ngati iwe. 40 Iweyo ukhala woyangʼanira nyumba yanga, ndipo anthu anga onse azimvera chilichonse chimene iweyo ungawauze.+ Koma ine ndekha ndikhala wamkulu kwa iwe chifukwa ndine mfumu.” 41 Farao anauzanso Yosefe kuti: “Tsopano ndikukuika kukhala woyangʼanira dziko lonse la Iguputo.”+

  • Genesis 41:48
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 48 Pa zaka 7 zimenezo, Yosefe anasonkhanitsa chakudya chonse chimene anakolola mʼdziko lonse la Iguputo nʼkuchisunga mʼmizinda. Mumzinda uliwonse, ankasunga chakudya chochokera mʼminda yozungulira mzindawo.

  • Genesis 45:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Choncho si inu amene munanditumiza kuno, koma ndi Mulungu woona. Anachita zimenezi kuti andiike kukhala nduna yaikulu ya* Farao, mbuye wa nyumba yake yonse ndiponso wolamulira wa dziko lonse la Iguputo.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena