Genesis 41:48 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 48 Pa zaka 7 zimenezo, Yosefe anasonkhanitsa chakudya chonse chimene anakolola m’dziko lonse la Iguputo, n’kuchisunga m’mizinda.+ Chakudya chonse chochokera m’minda yonse yozungulira mzinda uliwonse, anachisunga pakati pa mzindawo.+
48 Pa zaka 7 zimenezo, Yosefe anasonkhanitsa chakudya chonse chimene anakolola m’dziko lonse la Iguputo, n’kuchisunga m’mizinda.+ Chakudya chonse chochokera m’minda yonse yozungulira mzinda uliwonse, anachisunga pakati pa mzindawo.+