-
Genesis 41:48Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
48 Pa zaka 7 zimenezo, Yosefe anasonkhanitsa chakudya chonse chimene anakolola mʼdziko lonse la Iguputo nʼkuchisunga mʼmizinda. Mumzinda uliwonse, ankasunga chakudya chochokera mʼminda yozungulira mzindawo.
-